8 “Ndiyeno wodziyeretsayo azichapa zovala zake+ ndi kumeta tsitsi lake lonse, kenako azisamba+ ndipo azikhala woyera. Akatero, angathe kulowa mumsasa, koma azikhala kunja kwa hema wake masiku 7.+
23 Ndipo azibweretsa zimenezi kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako+ pamaso pa Yehova. Azibweretsa zinthuzi pa tsiku la 8+ kuti wansembe agamule kuti munthuyo ndi woyera.+