Levitiko 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Ndiyeno munthu akachira nthenda yake yakukhayo, pazipita masiku 7 kuti akhale woyera,+ kenako azichapa zovala zake ndi kusamba madzi otunga kumtsinje,+ ndipo iye azikhala woyera. Levitiko 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa tsiku la 8 azitenga njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda ndipo azibwera nazo pamaso pa Yehova, pakhomo la chihema chokumanako, ndi kupereka mbalamezo kwa wansembe. Numeri 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Kodi bambo ake akanam’lavulira+ malovu kumaso, sakanakhala wonyazitsidwa masiku 7? Choncho m’tulutseni+ akakhale kunja kwa msasa masiku 7,+ pambuyo pake mum’landire mumsasamo.”+
13 “‘Ndiyeno munthu akachira nthenda yake yakukhayo, pazipita masiku 7 kuti akhale woyera,+ kenako azichapa zovala zake ndi kusamba madzi otunga kumtsinje,+ ndipo iye azikhala woyera.
14 Pa tsiku la 8 azitenga njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda ndipo azibwera nazo pamaso pa Yehova, pakhomo la chihema chokumanako, ndi kupereka mbalamezo kwa wansembe.
14 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Kodi bambo ake akanam’lavulira+ malovu kumaso, sakanakhala wonyazitsidwa masiku 7? Choncho m’tulutseni+ akakhale kunja kwa msasa masiku 7,+ pambuyo pake mum’landire mumsasamo.”+