Levitiko 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ili likhale lamulo lokhudza wakhate+ pa tsiku limene adzam’bweretsa kwa wansembe kudzagamulidwa kuti ndi woyera.+ Levitiko 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako wansembe azidontheza+ magaziwo maulendo 7+ pamunthu amene akudziyeretsa ku khateyo, ndipo azigamula kuti munthuyo ndi woyera.+ Akatero, aziulutsa mbalame yamoyo ija pabwalo.+
2 “Ili likhale lamulo lokhudza wakhate+ pa tsiku limene adzam’bweretsa kwa wansembe kudzagamulidwa kuti ndi woyera.+
7 Kenako wansembe azidontheza+ magaziwo maulendo 7+ pamunthu amene akudziyeretsa ku khateyo, ndipo azigamula kuti munthuyo ndi woyera.+ Akatero, aziulutsa mbalame yamoyo ija pabwalo.+