Levitiko 16:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale,+ kuti machimo onse a ana a Isiraeli aziphimbidwa kamodzi pa chaka.”+ Motero, iye anachita monga mmene Yehova analamulira Mose.
34 Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale,+ kuti machimo onse a ana a Isiraeli aziphimbidwa kamodzi pa chaka.”+ Motero, iye anachita monga mmene Yehova analamulira Mose.