Levitiko 23:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Musamagwire ntchito iliyonse.+ Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale ku mibadwo yanu yonse, kulikonse kumene mungakhale. Numeri 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Pa tsiku la 10 la mwezi wa 7 umenewu, muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzidzisautsa.*+ Musamagwire ntchito yamtundu uliwonse.+
31 Musamagwire ntchito iliyonse.+ Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale ku mibadwo yanu yonse, kulikonse kumene mungakhale.
7 “‘Pa tsiku la 10 la mwezi wa 7 umenewu, muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzidzisautsa.*+ Musamagwire ntchito yamtundu uliwonse.+