Levitiko 23:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Pa tsiku loyambali muzitenga zipatso zabwino kwambiri, masamba a kanjedza,+ nthambi zikuluzikulu za masamba ambiri ndi mitengo ya msondodzi ya m’chigwa.* Mukatero muzisangalala+ kwa masiku 7 pamaso pa Yehova Mulungu wanu.
40 Pa tsiku loyambali muzitenga zipatso zabwino kwambiri, masamba a kanjedza,+ nthambi zikuluzikulu za masamba ambiri ndi mitengo ya msondodzi ya m’chigwa.* Mukatero muzisangalala+ kwa masiku 7 pamaso pa Yehova Mulungu wanu.