-
Nehemiya 8:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Analembamonso kuti azilengeza+ ndi kufuula m’mizinda yonse ndi mu Yerusalemu monse+ kuti: “Pitani kumapiri+ mukatenge nthambi za mitengo ya maolivi,+ nthambi za mitengo ya mafuta, nthambi za mitengo ya mchisu, masamba akanjedza ndi nthambi za mitengo ya masamba ambiri kuti mudzapangire misasa mogwirizana ndi zolembedwa.”
-
-
Chivumbulutso 7:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Zimenezi zitatha, nditayang’ana ndinaona khamu lalikulu la anthu,+ limene palibe munthu aliyense amene anatha kuliwerenga, lochokera m’dziko lililonse,+ fuko lililonse, mtundu uliwonse,+ ndi chinenero chilichonse.+ Iwo anali ataimirira pamaso pa mpando wachifumu+ ndi pamaso pa Mwanawankhosa, atavala mikanjo yoyera+ ndiponso atanyamula nthambi za kanjedza+ m’manja mwawo.
-