Levitiko 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ngati wolonjezayo ndi wosauka moti sangakwanitse mtengo woikidwiratuwo,+ azikaonetsa munthu woperekedwayo kwa wansembe, ndipo wansembe azinena mtengo wa munthuyo.+ Wansembe adzanena mtengo umene wolonjezayo angakwanitse.+
8 Koma ngati wolonjezayo ndi wosauka moti sangakwanitse mtengo woikidwiratuwo,+ azikaonetsa munthu woperekedwayo kwa wansembe, ndipo wansembe azinena mtengo wa munthuyo.+ Wansembe adzanena mtengo umene wolonjezayo angakwanitse.+