Numeri 2:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Alevi sanawawerenge+ pamodzi ndi ana a Isiraeli enawo, monga Yehova analamulira Mose.