Numeri 1:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma Alevi+ malinga ndi fuko la makolo awo sanawawerengere pamodzi ndi enawo.+ Numeri 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Uwerenge ana a Levi potsata nyumba ya makolo awo, malinga ndi mabanja awo. Uwerenge mwamuna aliyense kuyambira wamwezi umodzi kupita m’tsogolo.”+ Numeri 26:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Onse amene anawerengedwa pakati pa Alevi analipo 23,000. Amenewa anali amuna onse kuyambira amwezi umodzi kupita m’tsogolo.+ Iwowa sanawerengedwe limodzi ndi ana a Isiraeli,+ chifukwa sanafunikire kulandira cholowa pakati pa ana a Isiraeli.+
15 “Uwerenge ana a Levi potsata nyumba ya makolo awo, malinga ndi mabanja awo. Uwerenge mwamuna aliyense kuyambira wamwezi umodzi kupita m’tsogolo.”+
62 Onse amene anawerengedwa pakati pa Alevi analipo 23,000. Amenewa anali amuna onse kuyambira amwezi umodzi kupita m’tsogolo.+ Iwowa sanawerengedwe limodzi ndi ana a Isiraeli,+ chifukwa sanafunikire kulandira cholowa pakati pa ana a Isiraeli.+