Genesis 29:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Anakhalanso ndi pakati pena n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Apa tsopano mwamuna wanga andikonda basi, chifukwa ndamuberekera ana aamuna atatu.” Choncho mwanayo anamutcha Levi.*+ Genesis 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ana a Levi+ anali Gerisoni,+ Kohati+ ndi Merari.+ Numeri 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ine ndikutenga Alevi pakati pa ana a Isiraeli m’malo mwa ana onse oyamba kubadwa+ a ana a Isiraeli ndipo iwo akhala anga. 1 Mbiri 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ana a Levi+ anali Gerisoni,+ Kohati,+ ndi Merari.+
34 Anakhalanso ndi pakati pena n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Apa tsopano mwamuna wanga andikonda basi, chifukwa ndamuberekera ana aamuna atatu.” Choncho mwanayo anamutcha Levi.*+
12 “Ine ndikutenga Alevi pakati pa ana a Isiraeli m’malo mwa ana onse oyamba kubadwa+ a ana a Isiraeli ndipo iwo akhala anga.