Numeri 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mwa ana a Merari, panali banja la Amali+ ndi banja la Amusi.+ Awa ndiwo anali mabanja a Amerari.+ 1 Mbiri 6:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Ana a Merari+ potsata mabanja awo anapatsidwa mizinda kuchokera ku fuko la Rubeni,+ fuko la Gadi,+ ndi fuko la Zebuloni.+ Anapatsidwa mizinda 12 atachita maere.
63 Ana a Merari+ potsata mabanja awo anapatsidwa mizinda kuchokera ku fuko la Rubeni,+ fuko la Gadi,+ ndi fuko la Zebuloni.+ Anapatsidwa mizinda 12 atachita maere.