Numeri 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Uwu ndiwo utumiki umene mabanja a ana a Gerisoni+ azichita m’chihema chokumanako. Itamara+ mwana wa wansembe Aroni, ndiye aziyang’anira utumiki wawo.
28 Uwu ndiwo utumiki umene mabanja a ana a Gerisoni+ azichita m’chihema chokumanako. Itamara+ mwana wa wansembe Aroni, ndiye aziyang’anira utumiki wawo.