Numeri 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Azinyamulanso nsanamira+ zozungulira bwalo, zitsulo zokhazikapo nsanamirazo,+ zikhomo+ ndi zingwe zolimbitsira mpandawo limodzi ndi zipangizo zonse zimene amachitira utumiki wawo. Aliyense muzimugawira katundu woti azinyamula monga gawo lake.+
32 Azinyamulanso nsanamira+ zozungulira bwalo, zitsulo zokhazikapo nsanamirazo,+ zikhomo+ ndi zingwe zolimbitsira mpandawo limodzi ndi zipangizo zonse zimene amachitira utumiki wawo. Aliyense muzimugawira katundu woti azinyamula monga gawo lake.+