-
Numeri 6:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Wansembeyo atenge mwana mmodzi wa njiwa kapena wa nkhunda n’kumupereka monga nsembe yamachimo.+ Atengenso mwana wa njiwa kapena wa nkhunda winayo n’kumupereka monga nsembe yopsereza.+ Achite zimenezi kuti aphimbe machimo a munthuyo, popeza wachimwa pokhudza mtembo. Akatero aziyeretsa mutu wake pa tsikulo.
-