Levitiko 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mbalame inayo aziipereka ngati nsembe yopsereza motsatira ndondomeko ya nthawi zonse.+ Choncho wansembe aziphimba machimo+ amene munthuyo wachita, ndipo azikhululukidwa.+ Levitiko 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo+ ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza,+ azipereka imene angakwanitse pamodzi ndi nsembe yambewu. Pamenepo wansembe aziphimba machimo+ a munthu amene akudziyeretsayo pamaso pa Yehova.
10 Mbalame inayo aziipereka ngati nsembe yopsereza motsatira ndondomeko ya nthawi zonse.+ Choncho wansembe aziphimba machimo+ amene munthuyo wachita, ndipo azikhululukidwa.+
31 Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo+ ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza,+ azipereka imene angakwanitse pamodzi ndi nsembe yambewu. Pamenepo wansembe aziphimba machimo+ a munthu amene akudziyeretsayo pamaso pa Yehova.