Numeri 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Mnaziriyo azimeta tsitsi+ la kumutu kwake, lomwe ndi chizindikiro cha unaziri wake. Azilimetera pakhomo la chihema chokumanako. Akatero, azitenga tsitsi la mutu wake wa unazirilo, n’kuliponya pamoto umene uli pansi pa nsembe yachiyanjano.
18 “‘Mnaziriyo azimeta tsitsi+ la kumutu kwake, lomwe ndi chizindikiro cha unaziri wake. Azilimetera pakhomo la chihema chokumanako. Akatero, azitenga tsitsi la mutu wake wa unazirilo, n’kuliponya pamoto umene uli pansi pa nsembe yachiyanjano.