-
Machitidwe 21:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Utenge amuna amenewa+ ndipo ukachite mwambo wa kudziyeretsa pamodzi ndi iwo. Uwalipirire zonse zofunika,+ kuti amete tsitsi lawo.+ Ukatero, aliyense adzadziwa kuti mphekesera zimene anamva za iwe ndi nkhambakamwa chabe. Adzaona kuti ukuchita zinthu motsatira dongosolo, komanso kuti umasunga Chilamulo.+
-