Numeri 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo atsogoleri a Isiraeli,+ amene anali atsogoleri a nyumba za makolo awo, anapereka zopereka zawo.+ Anatero monga atsogoleri a mafuko awo, monganso oyang’anira anthu amene anawerengedwa aja.
2 Pamenepo atsogoleri a Isiraeli,+ amene anali atsogoleri a nyumba za makolo awo, anapereka zopereka zawo.+ Anatero monga atsogoleri a mafuko awo, monganso oyang’anira anthu amene anawerengedwa aja.