Numeri 7:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndipo za nsembe yachiyanjano,+ iye anapereka ng’ombe ziwiri, nkhosa zisanu zamphongo, mbuzi zisanu zamphongo, ndi ana a nkhosa asanu amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi. Izi n’zimene anapereka Selumiyeli mwana wa Zurisadai.+
41 Ndipo za nsembe yachiyanjano,+ iye anapereka ng’ombe ziwiri, nkhosa zisanu zamphongo, mbuzi zisanu zamphongo, ndi ana a nkhosa asanu amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi. Izi n’zimene anapereka Selumiyeli mwana wa Zurisadai.+