Numeri 7:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Iye anapereka ngʼombe ziwiri, nkhosa 5 zamphongo, mbuzi 5 zamphongo, ndi ana a nkhosa 5 amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi kuti zikhale za nsembe yamgwirizano.+ Izi nʼzimene Selumiyeli,+ mwana wa Zurisadai anapereka.
41 Iye anapereka ngʼombe ziwiri, nkhosa 5 zamphongo, mbuzi 5 zamphongo, ndi ana a nkhosa 5 amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi kuti zikhale za nsembe yamgwirizano.+ Izi nʼzimene Selumiyeli,+ mwana wa Zurisadai anapereka.