Numeri 7:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Pa tsiku la 8 panali mtsogoleri wa ana a Manase, Gamaliyeli+ mwana wa Pedazuri.