Numeri 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo iwo ananena kuti: “Ife ndife odetsedwa chifukwa takhudza mtembo wa munthu. Ngakhale kuti zili choncho, kodi tiyeneradi kuletsedwa kupereka nsembe+ kwa Yehova pakati pa ana a Isiraeli pa nthawi yake yoikidwiratu?”
7 Ndipo iwo ananena kuti: “Ife ndife odetsedwa chifukwa takhudza mtembo wa munthu. Ngakhale kuti zili choncho, kodi tiyeneradi kuletsedwa kupereka nsembe+ kwa Yehova pakati pa ana a Isiraeli pa nthawi yake yoikidwiratu?”