Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 7:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndipo munthu akakhudza chodetsa chilichonse, kaya chodetsa cha munthu+ kapena nyama yodetsedwa,+ kapenanso chinthu chilichonse chonyansa chodetsedwa,+ n’kudyako nyama ya nsembe yachiyanjano, imene ndi ya Yehova, munthu wotero aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.’”

  • Deuteronomo 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Uzipereka nsembe ya pasika kwa Yehova Mulungu wako.+ Uzipereka nkhosa ndi ng’ombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena