-
Levitiko 11:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Koma pa zamoyo za m’madzi zopezeka zambiri ndi pa zamoyo zina zonse za m’madzi, chilichonse chimene chilibe zipsepse ndi mamba, chopezeka m’nyanja ndi m’mitsinje, chikhale chonyansa kwa inu.
-