Ekisodo 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Inuyo muzikhala anthu oyera pamaso panga+ ndipo musadye nyama imene yaphedwa ndi chilombo kuthengo.+ Imeneyo muziponyera agalu.+ Levitiko 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mafuta a nyama yofa yokha ndi mafuta a nyama yokhadzulidwa ndi chilombo,+ mungawagwiritse ntchito ina iliyonse imene mungafune, koma musawadye ngakhale pang’ono. Levitiko 11:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Aliyense wakudya+ nyama yofa yokha azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo. Aliyense wonyamula nyama yakufayo azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.
31 “Inuyo muzikhala anthu oyera pamaso panga+ ndipo musadye nyama imene yaphedwa ndi chilombo kuthengo.+ Imeneyo muziponyera agalu.+
24 Mafuta a nyama yofa yokha ndi mafuta a nyama yokhadzulidwa ndi chilombo,+ mungawagwiritse ntchito ina iliyonse imene mungafune, koma musawadye ngakhale pang’ono.
40 Aliyense wakudya+ nyama yofa yokha azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo. Aliyense wonyamula nyama yakufayo azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.