Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 7:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma ngati nyama iliyonse ya nsembe yachiyanjano yadyedwa pa tsiku lachitatu, wopereka nsembeyo sadzayanjidwa ndi Mulungu.+ Nsembe yakeyo sadzapindula nayo.+ Idzakhala chinthu chonyansa, ndipo amene wadyako nsembeyo adzadziyankhira mlandu wa cholakwa chake.+

  • Deuteronomo 14:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Musadye chinthu chilichonse chonyansa.+

  • Yesaya 65:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 amene amakhala pansi kumanda,+ amene amakhala usiku wonse m’tinyumba ta alonda, amene amadya nyama ya nkhumba,+ ndipo m’miphika mwawo muli msuzi wa zinthu zodetsedwa.+

  • Yesaya 66:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Anthu amene akudzipatula ndi kudziyeretsa kuti apite kuminda+ n’kukaima kuseri kwa fano limene lili pakati pa mundawo, amene akudya nyama ya nkhumba+ ndi chinthu chonyansa, amene akudya ngakhale makoswe,+ onsewo adzathera limodzi,” akutero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena