Levitiko 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komanso nkhumba,+ chifukwa ziboda zake n’zogawanika ndipo zili ndi mpata pakati, koma siibzikula. Ikhale yodetsedwa kwa inu. Deuteronomo 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Musamadyenso nkhumba+ chifukwa ndi ya ziboda zogawanika koma sibzikula. Imeneyi ndi yodetsedwa kwa inu. Musamadye nyama yake ndipo ikafa musamaikhudze.+ Yesaya 65:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 amene amakhala pansi kumanda,+ amene amakhala usiku wonse m’tinyumba ta alonda, amene amadya nyama ya nkhumba,+ ndipo m’miphika mwawo muli msuzi wa zinthu zodetsedwa.+
7 Komanso nkhumba,+ chifukwa ziboda zake n’zogawanika ndipo zili ndi mpata pakati, koma siibzikula. Ikhale yodetsedwa kwa inu.
8 Musamadyenso nkhumba+ chifukwa ndi ya ziboda zogawanika koma sibzikula. Imeneyi ndi yodetsedwa kwa inu. Musamadye nyama yake ndipo ikafa musamaikhudze.+
4 amene amakhala pansi kumanda,+ amene amakhala usiku wonse m’tinyumba ta alonda, amene amadya nyama ya nkhumba,+ ndipo m’miphika mwawo muli msuzi wa zinthu zodetsedwa.+