Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 5:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Munthu akachimwa mwa kuchita chimodzi mwa zinthu zimene Yehova analamula kuti asachite, ngakhale kuti anachita mosazindikira,+ komabe wapalamula mlandu, pamenepo aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho.+

  • Levitiko 19:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndipo munthu wodya nyamayo aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho,+ chifukwa waipitsa chinthu chopatulika cha Yehova. Munthu wotero aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.

  • Numeri 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma ngati munthu ali wosadetsedwa, kapena sanapite pa ulendo, ndipo wanyalanyaza kukonza nsembe ya pasika, munthuyo aphedwe kuti asakhalenso pakati pa anthu ake,+ chifukwa sanapereke nsembeyo kwa Yehova pa nthawi yake yoikidwiratu. Munthuyo adzafa chifukwa cha kuchimwa kwake.+

  • Ezekieli 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako ine ndinati: “Chonde Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ine sindine woipitsidwa.+ Sindinadyepo nyama yopezeka itafa kapena nyama yochita kukhadzulidwa ndi chilombo kuyambira ndili mwana+ mpaka panopo, ndipo m’kamwa mwanga simunalowepo nyama yodetsedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena