Levitiko 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “‘Munthu akakhudza chinthu chodetsedwa, kaya ikhale nyama yakufa yakuthengo, nyama yakufa yoweta, kapena kamodzi mwa tizilombo topezeka tambiri,+ ngakhale kuti sanazindikire zotsatira zake,+ iye ndi wodetsedwa ndipo wapalamula mlandu.+ 1 Timoteyo 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Machimo a anthu ena amaonekera poyera,+ ndipo zimenezi zimachititsa kuti aweruzidwe. Koma anthu ena, machimo awo amadzaonekera pambuyo pake.+
2 “‘Munthu akakhudza chinthu chodetsedwa, kaya ikhale nyama yakufa yakuthengo, nyama yakufa yoweta, kapena kamodzi mwa tizilombo topezeka tambiri,+ ngakhale kuti sanazindikire zotsatira zake,+ iye ndi wodetsedwa ndipo wapalamula mlandu.+
24 Machimo a anthu ena amaonekera poyera,+ ndipo zimenezi zimachititsa kuti aweruzidwe. Koma anthu ena, machimo awo amadzaonekera pambuyo pake.+