Numeri 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova akalamula, iwo ankamanga msasa, ndipo Yehova akalamula, iwo ankanyamuka.+ Anali kumvera Yehova potsatira malangizo a Yehova odzera kwa Mose.+
23 Yehova akalamula, iwo ankamanga msasa, ndipo Yehova akalamula, iwo ankanyamuka.+ Anali kumvera Yehova potsatira malangizo a Yehova odzera kwa Mose.+