Ekisodo 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu ndi kuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Pamenepo anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+ Numeri 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngakhale mtambowo ukhale masiku ambiri pamwamba pa chihema, ana a Isiraeli ankamverabe Yehova, ndipo sankachoka pamalopo.+ Deuteronomo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nthawi zonse uzikonda Yehova Mulungu wako+ ndi kuchita zofuna zake, kutsatira mfundo zake, zigamulo zake+ ndi malamulo ake. Yoswa 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Simunawasiye abale anu masiku onsewa+ kufikira lero, ndipo mwasunga malamulo a Yehova Mulungu wanu.+
3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu ndi kuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Pamenepo anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+
19 Ngakhale mtambowo ukhale masiku ambiri pamwamba pa chihema, ana a Isiraeli ankamverabe Yehova, ndipo sankachoka pamalopo.+
11 “Nthawi zonse uzikonda Yehova Mulungu wako+ ndi kuchita zofuna zake, kutsatira mfundo zake, zigamulo zake+ ndi malamulo ake.
3 Simunawasiye abale anu masiku onsewa+ kufikira lero, ndipo mwasunga malamulo a Yehova Mulungu wanu.+