Numeri 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo ankanena kuti: “Kodi Yehova walankhula kudzera kwa Mose yekha? Kodi sanalankhulenso kudzera kwa ife?”+ Koma Yehova anali kumvetsera.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:2 Nsanja ya Olonda,10/15/2002, ptsa. 28-29
2 Iwo ankanena kuti: “Kodi Yehova walankhula kudzera kwa Mose yekha? Kodi sanalankhulenso kudzera kwa ife?”+ Koma Yehova anali kumvetsera.+