Numeri 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakhale malamulo ndi zigamulo zofanana kwa inu ndi kwa alendo amene akukhala nanu.’”+