Numeri 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Mose anakaika ndodozo pamaso pa Yehova m’chihema cha Umboni.+