Numeri 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano khamu lonse la ana a Isiraeli linafika m’chipululu cha Zini,+ m’mwezi woyamba, ndipo anthuwo anakhala ku Kadesi.+ Kumeneko n’kumene Miriamu+ anafera n’kuikidwa m’manda.
20 Tsopano khamu lonse la ana a Isiraeli linafika m’chipululu cha Zini,+ m’mwezi woyamba, ndipo anthuwo anakhala ku Kadesi.+ Kumeneko n’kumene Miriamu+ anafera n’kuikidwa m’manda.