Numeri 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Balamu anayankha atumiki a Balaki aja kuti: “Ngakhale Balaki atandipatsa nyumba yake yodzaza siliva ndi golide, sindingachite chilichonse mosemphana ndi zimene Yehova Mulungu wanga angandilamule, kaya kuchotsera kapena kuwonjezerapo.+
18 Koma Balamu anayankha atumiki a Balaki aja kuti: “Ngakhale Balaki atandipatsa nyumba yake yodzaza siliva ndi golide, sindingachite chilichonse mosemphana ndi zimene Yehova Mulungu wanga angandilamule, kaya kuchotsera kapena kuwonjezerapo.+