Numeri 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Buluyo ataonanso mngelo wa Yehova, tsopano anangokhala pansi, Balamu ali pamsana pake. Pamenepo Balamu anapsa mtima koopsa,+ ndipo anayamba kum’kwapulanso ndi ndodo yake.
27 Buluyo ataonanso mngelo wa Yehova, tsopano anangokhala pansi, Balamu ali pamsana pake. Pamenepo Balamu anapsa mtima koopsa,+ ndipo anayamba kum’kwapulanso ndi ndodo yake.