Numeri 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero Mose anauza oweruza a mu Isiraeli+ kuti: “Aliyense wa inu aphe+ anthu ake amene akukapembedza nawo Baala wa ku Peori.” Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:5 Nsanja ya Olonda,4/1/2004, tsa. 29
5 Chotero Mose anauza oweruza a mu Isiraeli+ kuti: “Aliyense wa inu aphe+ anthu ake amene akukapembedza nawo Baala wa ku Peori.”