Numeri 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Uwauze kuti, ‘Muzipereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto motere: Tsiku lililonse muzipereka nsembe yopsereza ya ana a nkhosa awiri amphongo, achaka chimodzi ndi opanda chilema.+
3 “Uwauze kuti, ‘Muzipereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto motere: Tsiku lililonse muzipereka nsembe yopsereza ya ana a nkhosa awiri amphongo, achaka chimodzi ndi opanda chilema.+