Numeri 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Muziperekanso mbuzi imodzi monga nsembe yamachimo, kuti ikhale yophimbira machimo anu.+