Numeri 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Muziperekanso mwana wa mbuzi+ monga nsembe yamachimo kwa Yehova, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe yake yachakumwa.+ Numeri 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi wamphongo, monga nsembe yamachimo yophimbira machimo anu.+
15 Muziperekanso mwana wa mbuzi+ monga nsembe yamachimo kwa Yehova, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe yake yachakumwa.+