Numeri 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Muzipereka nsembe zimenezi, kuwonjezera pa nsembe yopsereza+ ya m’mawa ya tsiku ndi tsiku.+