Numeri 29:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “‘Pa tsiku lachinayi, muzipereka ng’ombe 10 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo, ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, wopanda chilema.+
23 “‘Pa tsiku lachinayi, muzipereka ng’ombe 10 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo, ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, wopanda chilema.+