-
Numeri 29:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Pa tsiku limeneli muzipereka nsembe yopsereza+ yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova. Nsembe imeneyo izikhala ya ng’ombe 13 zazing’ono zamphongo, nkhosa zamphongo ziwiri, ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi. Muzionetsetsa kuti nyamazi n’zopanda chilema.+
-