Numeri 31:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi mwaiwala kuti akaziwa ndi amene anatsatira mawu a Balamu? Si ndiwo kodi amene ananyengerera ana a Isiraeli kuti achimwire Yehova pa zochitika za ku Peori,+ kuti mliri ugwere khamu la anthu a Yehova?+
16 Kodi mwaiwala kuti akaziwa ndi amene anatsatira mawu a Balamu? Si ndiwo kodi amene ananyengerera ana a Isiraeli kuti achimwire Yehova pa zochitika za ku Peori,+ kuti mliri ugwere khamu la anthu a Yehova?+