Numeri 31:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pajatu akazi amenewa ndi amene anatsatira mawu a Balamu nʼkunyengerera Aisiraeli kuti achimwire Yehova+ pa zimene zinachitika ku Peori,+ moti mliri unagwera gulu la anthu a Yehova.+
16 Pajatu akazi amenewa ndi amene anatsatira mawu a Balamu nʼkunyengerera Aisiraeli kuti achimwire Yehova+ pa zimene zinachitika ku Peori,+ moti mliri unagwera gulu la anthu a Yehova.+