Numeri 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Fuko la ana a Rubeni mwa mabanja a makolo awo, ndi fuko la ana a Gadi mwa mabanja a makolo awo, alandira kale cholowa chawo. Ndiponso hafu ya fuko la Manase, nawonso alandira kale cholowa chawo.+
14 Fuko la ana a Rubeni mwa mabanja a makolo awo, ndi fuko la ana a Gadi mwa mabanja a makolo awo, alandira kale cholowa chawo. Ndiponso hafu ya fuko la Manase, nawonso alandira kale cholowa chawo.+