Numeri 34:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amenewa ndiwo amuna amene Yehova analamula kuti akagawire malo ana a Isiraeli, kuti akakhale ndi malo awoawo m’dziko la Kanani.+
29 Amenewa ndiwo amuna amene Yehova analamula kuti akagawire malo ana a Isiraeli, kuti akakhale ndi malo awoawo m’dziko la Kanani.+