Deuteronomo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo masiku amene tinayenda kuchokera ku Kadesi-barinea mpaka kuwoloka chigwa cha Zeredi anali zaka 38, kufikira m’badwo wa amuna otha kupita kunkhondo utatha pakati panu, monga mmene Yehova analumbirira kwa iwo.+
14 Ndipo masiku amene tinayenda kuchokera ku Kadesi-barinea mpaka kuwoloka chigwa cha Zeredi anali zaka 38, kufikira m’badwo wa amuna otha kupita kunkhondo utatha pakati panu, monga mmene Yehova analumbirira kwa iwo.+